

Translation of the Customary
GAWO I – MAYAMBIDWE NDI KUGWIRITSA NTCHITO KWA LAMULO 1. Lamulo ili ndi Lamulo la Malo Amakolo, 2016. GAWO II – KAYANG’ANIRIDWE KA MALO AMAKOLO 2. Malo amakolo ndi malo onse amene– a) ali mudera lomwe limayang’aniridwa ndi Mfumu ya Ndodo; b) malire ake anakhazikitsidwa ndi Komiti yoyang’anira malo amakolo ku dera-lo; kapena c) ali ndi chiphaso choperekedwa ndi Mkulu woyang’anira za Malo mu Unduna wa za Malo. 3. (1) Chiphaso cha malo amakolo a) chiperekedwe mu dzina la Mfumu ya Ndodo; b) chimapereka mphamvu kwa Komiti yoyamg’anira za malo amakolo pakayendetsedwe ka malowo; c) chimapereka umboni kuti anthu wonse amene ali pa malo amakolowo ndiwololedwa kukhala pamalowo motsatira mwambo waderalo. (2) Mfumu ya Ndodo yili ndi udindo wosunga chiphaso cha dera lake mosamala. (3) Malire a malo amene ali pansi pa ulamuliro wa Mfumu ya Ndodo sangasinthidwe popanda chilolezo cha Mkulu woyang’anira za malo ku Unduna wa za Malo. (4) Mkulu woyang’anira za malo ku Unduna wa za Malo ali ndi udindo wosunga kalembera wa malo onse amene ali pa ulamuliro wa Mfumu ya Ndodo.
Land Act, 2016 and the Customary
Land Regulations, 2018
Author: Chikosa M. SILUNGWE, PhD
Assignment: FAO Gcp/Glo/347/MUL
26.08.19
Date of Finalization: 10.03.20
Authors and Publishers
Chikosa M. SILUNGWE, PhD
The Food and Agriculture Organization of the United Nations leads international efforts to defeat hunger. Serving both developed and developing countries, FAO acts as a neutral forum where all nations meet as equals to negotiate agreements and debate policy. FAO is also a source of knowledge and information.
Wikipedia:
"Under the 1995 constitution, the president, who is both chief of state and head of the government, is chosen through universal direct suffrage every 5 years. Malawi has a vice president who is elected with the president. The president has the option of appointing a second vice president, who must be from a different party. It also includes a presidentially appointed cabinet. The members of the cabinet of Malawi can be drawn from either within or outside of the legislature."